Deuteronomy 1:35 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mu mbadwo woipitsitsawu palibe ndi mmodzi yemwe amene adzaloŵe m'dziko lachondelo limene ndidalumbira kuti ndidzapatsa makolo anu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Palibe mmodzi wa anthu awa a mbadwo uno woipa adzaona dziko lokomalo ndinalumbira kupatsa makolo anuli.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Palibe ndi mmodzi yemwe mwa mʼbado woyipawu amene adzaona dziko labwino limene ndinalumbira kupatsa makolo anu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Palibe mmodzi wa anthu awa a mbadwo uno woipa adzaona dziko lokomalo ndinalumbira kupatsa makolo anuli.