Deuteronomy 1:37 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adandikwiyira inenso chifukwa cha inu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova anakwiya ndi inenso chifukwa cha inu, ndi kuti, Iwenso sudzalowamo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa cha inu, Yehova anakwiyiranso ine ndipo anati, “Iwenso sudzalowa mʼdzikomo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova anakwiya ndi inenso cifukwa ca inu, ndi kuti, lwenso sudzalowamo.