Deuteronomy 1:38 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adati, “Iwe Mose sudzaloŵa m'dzikomo, koma mthandizi wako Yoswa, mwana wa Nuni, ndiye adzaloŵe. Umlimbitse mtima Yoswayo, poti iyeyo ndiye adzatsogolere Aisraele pokaloŵa m'dzikomo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yoswa mwana wa Nuni, wakuima pamaso pako, iye adzalowamo; umlimbitse mtima; popeza iye adzalandiritsa Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Yoswa mwana wa Nuni amene amakuthandiza, adzalowa mʼdzikomo. Umulimbikitse chifukwa adzatsogolera Israeli kukalandira dzikolo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yoswa mwana wa Nuni, wakuima pamaso pako, iye adzalowamo; umlimbitse mtima; popeza iye adzalandiritsa Israyeli.