Deuteronomy 1:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zimenezi zidachitika Moseyo atagonjetsa kale Sihoni mfumu ya Aamori, amene ankakhala ku Hesiboni, ndi mfumu Ogi wa ku Basani, amene ankakhala ku Asitaroti ndi ku Ederei.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
atakantha Sihoni mfumu ya Aamori, wakukhala m'Hesiboni, ndi Ogi mfumu ya Basani, wakukhala m'Asitaroti, ku Ederei.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Apa nʼkuti atagonjetsa Sihoni mfumu ya Aamori, amene amalamulira ku Hesiboni, ndipo pa Ederi anagonjetsa Ogi mfumu ya ku Basani, amene amalamulira mu Asiteroti.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
atakantha Sihoni mfumu ya Aamori, wakukhala m'Hesiboni, ndi Ogi mfumu ya Basana, wakukhala m'Asitaroti, ku Edrei.