Deuteronomy 1:40 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma inu bwererani, muzipita ku chipululu, kulunjika ku Nyanja Yofiira.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma inu, bwererani, mukani ulendo wanu kuchipululu, njira ya ku Nyanja Yofiira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma inu, tembenukani nyamukani kulowera cha ku chipululu kutsatira njira ya ku Nyanja Yofiira.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma inu, bwererani, mukani ulendo wanu kucipululu, njira ya ku Nyanja Yofiira.