Deuteronomy 1:45 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono inu pobwera mudalira kuti Chauta akuthandizeni, koma Chauta sadakumvereni kapena kukutcherani khutu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo munabwerera ndi kulira pamaso pa Yehova; koma Yehova sanamvere mau anu, kapena kukutcherani khutu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munabwererako mukulira pamaso pa Yehova, koma Iye sanalabadire kulira kwanuko ndipo sanakumvetsereni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo munabwerera ndi kulira pamaso pa Yehova; koma Yehova sanamvera mau anu, kapena kukucherani khutu.