Deuteronomy 1:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mose adayamba kufotokozera anthu malamuloŵa ku tsidya la Yordani m'dziko la Mowabu, adati:
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsidya lija la Yordani, m'dziko la Mowabu, Mose anayamba kufotokozera chilamulo ichi, ndi kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chakummawa kwa Yorodani mʼchigawo cha Mowabu, Mose anayamba kufotokozera lamulo ili kunena kuti:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsidya lija la Yordano, m'dziko la Moabu, Mose anayamba kufotokozera cilamulo ici, ndi kuti.