Deuteronomy 1:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene tinali ku phiri la Horebu, Chauta, Mulungu wathu, adatiwuza kuti, “Inu mwakhalitsa kuphiri kuno.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova Mulungu wathu ananena ndi ife m'Horebu, ndi kuti Yakwanira nthawi yokhala inu m'phiri muno;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ku Horebu, Yehova Mulungu wathu anati kwa ife, “Mwakhalitsa pa phiri lino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova Mulungu wathu ananena ndi ife m'Horebe, ndi kuti, Yakwanira nthawi yokhala inu m'phiri muno;