Deuteronomy 1:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndi limenelitu dziko limene ndikulipereka kwa inu. Muloŵe ndi kukhazikika m'dzikoli limene Ine Chauta, Mulungu wanu, ndidalumbira kuti ndidzapatsa makolo anu, Abrahamu, Isaki ndi Yakobe, ndi zidzukulu zao zonse.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, ndakupatsani dzikoli pamaso panu, lowani landirani dziko limene Yehova analumbirira makolo anu, Abrahamu, Isaki, ndi Yakobo, kuti ili ndidzawapatsa iwo ndi mbeu zao pambuyo pao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Taonani, Ine ndakupatsani dziko ili. Lowani ndi kulilanda dziko limene Yehova analumbira kuti adzapereka kwa makolo anu, Abrahamu, Isake ndi Yakobo komanso kwa zidzukulu zawo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, ndakupatsani dzikoli pamaso panu, lowani landirani dziko limene Yehova analumbirira makolo anu, Abrahamu, Isake, ndi Yakobo, kuti ili ndidzawapatsa iwo ndi mbeu zao pambuyo pao.