Deuteronomy 1:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mose adatinso: Paja ndidakuuzani nthaŵi imeneyo kuti sindingathe kusenza ndekha udindo wokutsogolerani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo muja ndinanena ndi inu, ndi kuti, Sinditha ine kukunyamulani ndekha;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa nthawi imeneyi ine ndinati kwa inu, “Inu ndinu katundu olemera kwambiri woti sindingathe kumunyamula ndekha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo muja ndinanena ndi inu, ndi kuti, Sinditha ine kukunyamulani ndekha;