Deuteronomy 10:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adandiwuza kuti ndipite nanu, ndikhale mtsogoleri wanu, kuti potero muloŵe ndi kukhazikika m'dziko limene Iye adalumbira kuti adzapatsa makolo anu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehova anati kwa ine, Uka, tenga ulendo pamaso pa anthu; kuti alowe ndi kulandira dzikoli ndinalumbirira makolo ao kuti ndidzawapatsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova anati kwa ine, “Pita ndi kutsogolera anthuwa pa njira yawo, kuti alowe ndi kulandira dziko limene ndinalumbira kwa makolo awo kuti ndiwapatse.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehova anati kwa ine, Uka, tenga ulendo pamaso pa anthu; kuti alowe ndi kulandira dzikoli ndinalumbirira makolo ao kuti ndidzawapatsa.