Deuteronomy 10:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe Chauta adakonda makolo anu kwambiri, kotero kuti m'malo mwa kusankha anthu ena, adasankha zidzukulu za makolo anuwo, ndiye kuti inuyo, mpaka lero lino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Yehova anakondwera nao makolo anu kuwakonda, nasankha mbeu zao zakuwatsata, ndiwo inu, mwa mitundu yonse ya anthu, monga kuli lero lino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova anayika mtima wake pa makolo anu okha ndipo anawakondadi nasankha adzukulu awo mwa mitundu yonse pa dziko lapansi, kunena inuyo monga mulili lero.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Yehova anakondwera nao makolo anu kuwakonda, nasankha mbeu zao zakuwatsata, ndiwo inu, mwa mitundu yonse ya anthu, monga kuli lero lino.