Deuteronomy 10:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono muŵakonde anthu achilendowo, chifukwa paja inunso mudaali alendo ku Ejipito.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
M'mwemo mukondane naye mlendo; popeza munali alendo m'dziko la Ejipito.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Muzikonda alendo popeza inuyo munali alendo mʼdziko la Igupto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'mwemo mukondane naye mlendo; popeza munali alendo m'dziko la Aigupto.