Deuteronomy 10:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene makolo anu ankapita ku Ejipito, adaalipo makumi asanu ndi aŵiri okha. Koma tsopano Chauta, Mulungu wanu, wakuchulukitsani ngati nyenyezi zamumlengalenga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Makolo anu anatsikira ku Ejipito ndiwo anthu makumi asanu ndi awiri; ndipo Yehova Mulungu wanu anakusandulizani tsopano muchuluke ngati nyenyezi za kumwamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Makolo anu amene anapita ku Igupto analipo makumi asanu ndi awiri onse pamodzi, ndipo tsopano Yehova Mulungu wanu wakuchulukitsani ngati nyenyezi zakumwamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Makolo anu anatsikira ku Aigupto ndiwo anthu makumi asanu ndi awiri; ndipo Yehova Mulungu wanu anakusandulizani tsopano mucuruke ngati nyenyezi za kumwamba.