Deuteronomy 10:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pompo ndidapanga bokosi la mtengo wakasiya, ndipo ndidasemanso miyala iŵiri monga yoyamba ija, ndipo ndidakwera phiri, nditatenga miyalayo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Potero ndinapanga likasa la mtengo wakasiya, ndinasemanso magome awiri amiyala onga oyamba aja, ndi kukwera m'phirimo, magome awiri ali m'manja mwanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho ndinapanga bokosi lamatabwa amtengo wa mkesha ndi kusema miyala iwiri yofanana ndi yoyamba ija, ndipo ndinapita ku phiri nditanyamula miyala iwiri mʼmanja mwanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Potero ndinapanga likasa la mtengo wasitimu, ndinasemanso magome awiri amiyala onga oyamba aja, ndi kukwera m'phirimo, magome awiri ali m'manja mwanga.