Deuteronomy 10:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo Chauta adalemba pa miyalayo mau omwewo amene adaalemba pa miyala ija. Mauwo ndiwo malamulo khumi amene adakupatsani pamene adalankhula nanu m'moto muja, pa tsiku limene mudasonkhana nonse kuphiri kuja. Chauta adandipatsa miyalayo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo analembera pamagome, monga mwa malembedwe oyamba, mau khumiwo, amene Yehova adanena ndi inu m'phirimo, ali pakati pa moto, tsiku la kusonkhanako; ndipo Yehova anandipatsa awa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova analemba pa miyala iwiriyo zimene analemba poyamba, Malamulo Khumi amene analengeza kwa inu pa phiri paja, mʼmoto, pa tsiku la msonkhano. Ndipo Yehova anawapereka kwa ine.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo analembera pamagome, monga mwa malembedwe oyamba, mau khumiwo, amene Yehova adanena ndi inu m'phirimo, ali pakati pa moto, tsiku la kusonkhanako; ndipo Yehova anandipatsa awa.