Deuteronomy 10:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake fuko la Levi silidalandireko dziko kapena choloŵa monga mafuko ena aja. Chauta ndiye choloŵa chao, monga momwe Chauta, Mulungu wanu, adalonjezera.)
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake Levi alibe gawo kapena cholowa pamodzi ndi abale ake; Yehova mwini wake ndiye cholowa chake, monga Yehova Mulungu wake ananena naye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chake Alevi alibe gawo kapena cholowa pakati pa abale awo. Yehova ndiye cholowa chawo monga momwe Yehova Mulungu wanu anawawuzira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace Levi alibe gawo kapena colowa pamodzi ndi abale ace; Yehova mwini wace ndiye colowa cace, monga Yehova Mulungu wace ananena naye.