Deuteronomy 11:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Muzikonda Chauta, Mulungu wanu, ndipo nthaŵi zonse muzimvera malamulo ndi malangizo ake onse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake muzikonda Yehova Mulungu wanu, ndi kusunga chilangizo chake, ndi malemba ake, ndi maweruzo ake, ndi malamulo ake, masiku onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Muzikonda Yehova Mulungu wanu ndipo nthawi zonse muzitsata zimene Iyeyo anakulamulani, malangizo, zikhazikitso ndi malamulo ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace muzikonda Yehova Mulungu wanu, ndi kusunga cilangizo cace, ndi malemba ace, ndi maweruzo ace, ndi malamulo ace, masiku onse.