Deuteronomy 11:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta, Mulungu wanu, ndiye amene amasamalira dziko limenelo ndi kumaliyang'anira chaka chonse mosalekeza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndilo dziko loti Yehova Mulungu wanu alisamalira, maso a Yehova Mulungu wanu akhalapo chikhalire, kuyambira chaka mpaka kutsiriza chaka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ili ndi dziko limene Yehova Mulungu wanu amalisamalira. Maso a Yehova Mulungu wanu amaliyangʼanira nthawi zonse kuchokera ku mayambiriro a chaka mpaka kumapeto kwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndilo dziko loti Yehova Mulungu wanu alisamalira, maso a Yehova Mulungu wanu akhalapo cikhalire, kuyambira caka mpaka kutsiriza caka.