Deuteronomy 11:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo Iye azidzagwetsa mvula m'dziko mwanu pa nthaŵi yake, monga nthaŵi yadzinja ndiponso nthaŵi yachilimwe, kotero kuti mudzakhala ndi tirigu wambiri, vinyo wambiri ndiponso mafuta aolivi ambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndidzapatsa mvula ya dziko lanu m'nyengo yake, ya chizimalupsa ndi ya masika, kuti mutute tirigu wanu, ndi vinyo wanu, ndi mafuta anu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pamenepo ndidzatumiza mvula mʼdziko mwanu pa nthawi yake mʼnyengo ya dzinja ndi chilimwe, kuti mudzakolole tirigu wambiri ndi kuti mudzakhale ndi vinyo watsopano ndi mafuta.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndidzapatsa mvula ya dziko lanu m'nyengo yace, ya myundo ndi ya masika, kuti mutute tirigu wanu, ndi vinyo wanu, ndi mafuta anu.