Deuteronomy 11:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo inu ndi ana anu, mudzakhala ndi moyo nthaŵi yaitali m'dziko limene Chauta, Mulungu wanu, adalumbira kuti adzapatsa makolo anu. Mudzakhala m'dziko limenelo nthaŵi zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti masiku anu ndi masiku a ana anu achuluke m'dziko limene Yehova analumbira kwa makolo anu kuti adzawapatsali, monga masiku a thambo lili pamwamba pa dziko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuti inu ndi ana anu mukhale mʼdziko limene Yehova analumbira kupatsa makolo anu mpaka kalekale monga umakhalira mlengalenga pamwamba pa dziko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti masiku anu ndi masiku a ana anu acuruke m'dziko limene Yehova analumbira kwa makolo anu kuti adzawapatsali, monga masiku a thambo liri pamwamba pa dziko.