Deuteronomy 11:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono pamene inu mukupita, Chauta adzapirikitsa mitundu ina yonseyo, ndipo mudzalanda maiko a mitundu ya anthu akuluakulu ndi amphamvu kupambana inu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova adzapirikitsa amitundu awa onse pamaso panu, ndipo mudzalanda amitundu akulu ndi amphamvu oposa inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova adzapirikitsa mitundu ina yonseyi inu musanafike ndipo mudzagonjetsa mitundu ikuluikulu ndi yamphamvu kuposa inu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova adzapitikitsa amitundu awa onse pamaso panu, ndipo mudzalanda amitundu akuru ndi amphamvu oposa inu.