Deuteronomy 11:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Lero ndikukupatsani zinthu ziŵiri kuti musankhepo, madalitso kapena matemberero.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, ndilikuika pamaso panu lero dalitso ndi temberero;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Taonani, lero ndikuyika dalitso ndi temberero pakati panu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, ndirikuika pamaso panu lero dalitso ndi temberero;