Deuteronomy 11:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudaona zizindikiro ndi ntchito zimene Chauta adachita polanga Farao ndi dziko lake lonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi zizindikiro zake, ndi ntchito zake, adazichitira Farao mfumu ya Aejipito, ndi dziko lake lonse pakati pa Ejipito;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
zizindikiro zozizwitsa zimene anazionetsa ndi zinthu zimene anazichita mʼkati mwa Igupto, Farao mfumu ya Igupto ndi kwa dziko lake lonse;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi zizindikilo zace, ndi nchito zace, adazicitira Farao mfumu ya Aigupto, ndi dziko lace lonse pakati pa Aigupto;