Deuteronomy 11:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Muli pafupi kuwoloka Yordani ndi kukakhalamo m'dziko limene Chauta, Mulungu wanu, akukupatsani. Mukakalilandira ndi kukhalamo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti mulinkuoloka Yordani kulowa ndi kulandira dziko limene Yehova Mulungu wanu akupatsani; ndipo mudzachilandira cholowa chanu, ndi kukhalamo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwatsala pangʼono kuwoloka Yorodani kuti mulowe ndi kutenga dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani. Mukadzalitenga dzikolo ndi kukhalamo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mulinkuoloka Yordano kulowa ndi kulandira dziko limene Yehova Mulungu wanu akupatsani; ndipo mudzacilandira colowa canu, ndi kukhalamo.