Deuteronomy 11:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudzakhaladi nthaŵi yaitali m'dziko lamwanaalirenjilo, limene Chauta adalumbira kuti adzapatsa makolo anu ndi zidzukulu zao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kuti masiku anu achuluke m'dziko limene Yehova analumbirira makolo anu, kuti adzawapatsa iwo ndi mbeu zao, dziko moyenda mkaka ndi uchi ngati madzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndiponso kuti mukhalitse mʼdziko limene Yehova analumbira kupatsa makolo anu ndi zidzukulu zawo, lomwe ndi dziko loyenda mkaka ndi uchi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi kuti masiku anu acuruke m'dziko limene Yehova analumbirira makolo anu, kuti adzawapatsa iwo ndi mbeu zao, dziko moyenda mkaka ndi uci ngati madzi.