Deuteronomy 12:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Magazi okha a nyamazo musadzadye, koma muzikaŵataya pansi ngati madzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwazi wao wokha musamadya; muziuthira panthaka ngati madzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma musamadye magazi. Muziwathira pansi ngati madzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwazi wao wokha musamadya; muziuthira panthaka ngati madzi.