Deuteronomy 12:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Muchenjere kuti, nthaŵi zonse mudzakhale m'dzikomo, musadzaiŵale Alevi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Dzichenjerani nokha, musataye Mlevi masiku onse akukhala inu m'dziko mwanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Muonetsetse kuti musawataye Alevi pa masiku onse amene mukhale mʼdziko lanumo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Dzicenjerani nokha, musataye Mlevi masiku onse akukhala inu m'dziko mwanu.