Deuteronomy 12:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aliyense woipitsidwa pa zachipembedzo kapena wosaipitsidwa adyeko nyamayo, monga momwe akadadyera nyama yamphoyo kapena yangondo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma monga umo amadya mphoyo ndi ngondo momwemo uzizidya; odetsa ndi oyera adyeko chimodzimodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Muzidye ngati mukudya gwape kapena mbawala. Onse oyeretsedwa monga mwa mwambo ndi osayeretsedwa omwe akhoza kudya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma monga umo amadya mphoyo ndi ngondo momwemo uzizidya; odetsa ndi oyera adyeko cimodzimodzi.