Deuteronomy 12:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Magazi okha musadye podya nyamayo, chifukwa moyo uli m'magazimo, motero inu musadye moyowo pamodzi ndi nyamayo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma mulimbikepo ndi kusadya mwaziwo; popeza mwazi ndiwo moyo, nimusamadya moyo pamodzi ndi nyama yake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma muonetsetse kuti musadye magazi, chifukwa magazi ndi moyo, ndipo musamadye moyo pamodzi ndi nyama.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma mulimbikepo ndi kusadya mwaziwo; popeza mwazi ndiwo moyo, nimusamadya moyo pamodzi ndi nyama yace.