Deuteronomy 12:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mukapanda kudya magaziwo, zonse zidzakuyenderani bwino inuyo ndi zidzukulu zanu, chifukwa cha kuchita zabwino motere pamaso pa Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Musamadya uwu; kuti chikukomereni inu, ndi ana anu akudza m'mbuyo mwanu, pakuchita inu zoyenera pamaso pa Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Musamadye magazi kuti zikuyendereni bwino inu pamodzi ndi ana anu a pambuyo panu, popeza mudzakhala mukuchita zoyenera pamaso pa Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Musamadya uwu; kuti cikukomereni inu, ndi ana anu akudza m'mbuyo mwanu, pakucita inu zoyenera pamaso pa Yehova.