Deuteronomy 12:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zopereka zanu zimene mudapatulira Chauta pamodzi ndi mphatso zanu zimene mudalonjeza, zonsezo mupite nazo kwa Chauta pa malo achipembedzo amene adzaŵasankha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zopatulika zanu zokha zimene muli nazo, ndi zowinda zanu, muzitenge, ndi kupita nazo ku malo amene Yehova adzasankha;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma mutenge zinthu zanu zoyeretsedwa ndi china chilichonse chimene munalumbira kupereka, ndi kupita kumalo kumene Yehova adzasankhe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zopatulika zanu zokha zimene muli nazo, ndi zowinda zanu, muzitenge, ndi kupita nazo ku malo amene Yehova adzasanka;