Deuteronomy 12:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵi imeneyo ikadzafika, musadzachite m'mene timachitira kunomu. Mpaka tsopano lino, aliyense mwa inu amangopembedza monga akufunira,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Musamadzichita monga mwa zonse tizichita kuno lero, yense kuchita chilichonse chiyenera m'maso mwake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Musadzachite monga tikuchitira lero lino, aliyense kumachita zimene akuona kuti ndi zoyenera,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Musamadzacita monga mwa zonse tizicita kuno lero, yense kucita ciri conse ciyenera m'maso mwace;