Deuteronomy 12:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
poti simunaloŵebe m'dziko limene Chauta, Mulungu wanu, akukupatsani ngati choloŵa chanu, kumene mudzatha kukhala mwamtendere.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti mpaka lero simunafikira mpumulo ndi cholowa, zimene Yehova Mulungu wanu adzakupatsani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pakuti simunafike ku malo opumulirako ndi ku cholowa chimene Yehova Mulungu wanu akukupatsani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti mpaka lero simunafikira mpumulo ndi colowa, zimene Yehova Mulungu wanu adzakupatsani.