Deuteronomy 15:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
malinga mukamamvera mau ake ndi kusamala zotsata malamulo amene ndikukulamulani leroŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chokhachi mumvere chimverere mau a Yehova Mulungu wanu, kuti musamalire kuchita malamulo awa onse amene ndikuuzani lero lino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Adzakudalitsani pokhapokha ngati mudzamveradi Yehova Mulungu wanu posunga ndi kutsatira malamulo onse amene ndikukupatsani lero.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
cokhaci mumvere cimverere mau a Yehova Mulungu wanu, kuti musamalire kucita malamulo awa onse amene ndikuuzani lero lino.