Deuteronomy 15:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Makamaka muzidzamchitira chifundo ndi kumkongoza monga momwe angafunire.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma muzimtansira dzanja lanu ndithu ndi kumkongoletsa ndithu zofikira kusowa kwake, monga umo amasowa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma mukhale ofewa manja ndipo mumukongoze mʼbale wanu momasuka pa chilichonse chimene akufuna.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma muzimtansira dzanjalanundithu ndi kumkongoletsa ndithu zofikira kusowa kwace, monga umo amasowa.