Deuteronomy 16:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Muziphika nyamayo ndi kuidyera pa malo achipembedzo amodziwo, ndipo muzibwerera ku zithando zanu m'maŵa mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo muiphike ndi kuidya m'malo amene Yehova Mulungu wanu adzasankha; koma m'mawa mwake mubwerere kunka ku mahema anu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Muyiwotche ndi kuyidya pa malo pamene Yehova Mulungu wanu adzasankhe. Kenaka mmawa mubwerere ku matenti anu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo muiphike ndi kuidya m'malo amene Yehova Mulungu wanu adzasankha; koma m'mawa mwace mubwerere kumka ku mahema anu.