Deuteronomy 17:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwowo atagamula, inu muyenera kungochita zomwe akuuzani ku malo osankhidwa ndi Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo muchite monga momwe ananena mau akufotokozeraniwo, ku malo amene Yehova adzawasankha; nimusamalire kuchita monga mwa zonse akulangizanizi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kachiteni zimene adzakuwuzenizo kuchokera ku malo amene Yehova adzasankhe. Kaonetsetseni kuti mukutsatira zonse zimene akuwuzanizo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mucite monga momwe ananena mau akufotokozeraniwo, ku malo amene Yehova adzawasankha; nimusamalire kucita monga mwa zonse akulangizanizi,