Deuteronomy 17:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Buku limeneli adzalisunge ndipo azidzaŵerengamo pa moyo wake wonse, kuti adzaphunzire kuwopa Chauta, Mulungu wake, pakutsata mokhulupirika zonse zolembedwa m'bukumo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo azikhala nacho, nawerengemo masiku onse a moyo wake; kuti aphunzire kuopa Yehova Mulungu wake, kusunga mau onse a chilamulo ichi ndi malemba awa, kuwachita;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Asunge zimene walembazo ndipo ayenera kumaziwerenga masiku onse a moyo wake, kuti aphunzire kuopa Yehova Mulungu wake posunga mosamalitsa malamulo ndi malangizowa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo azikhala naco, nawerengemo masiku onse a moyo wace; kuti aphunzire kuopa Yehova Mulungu wace, kusunga mau ons acilamulo ici ndi malemba awa, kuwacita;