Deuteronomy 17:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndipo mupereke mlandu wanuwo kwa ansembe Achilevi ndi kwa muweruzi amene ali pa ntchito pa nthaŵi imeneyo. Ndipo iwowo agamule mlanduwo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nimufike kwa ansembe, Alevi, ndi kwa woweruza wa m'masiku awo; nimufunsire; ndipo adzakufotokozerani maweruzidwe ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mudzapite kwa ansembe Alevi ndi kwa woweruza wa pa nthawi imeneyo. Kawafunseni ndipo iwowo adzakuwuzani zoyenera kuchita.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nimufike kwa ansembe, Alevi, ndi kwa woweruza wa m'masiku awo; nimufunsire; ndipo adzakufotokozerani maweruzidwe ace.