Deuteronomy 19:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zikatero, akuluakulu akwao adzamuitanitse kuchokera ku mzinda wakewo, ndi kukampereka kwa woyenera kumlipsira uja kuti aphedwe ndithu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pamenepo akulu a mudzi wake atumize ndi kumtengako ndi kumpereka m'manja mwa wolipsa mwazi, kuti afe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
akuluakulu a mu mzinda wake akamugwire ndi kumubwezera ku mzinda wake namupereka kwa wolipsira kuti aphedwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pamenepo akuru a mudzi wace atumize ndi kumtengako ndi kumpereka m'manja mwa wolipsa mwazi, kuti afe.