Deuteronomy 19:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu wina akaneneza mnzake momnamizira kuti walakwa,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mboni yachiwawa ikaukira munthu kumneneza ndi kuti analakwa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati mboni yonama ifuna kunamizira munthu mlandu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mboni yaciwawa ikaukira munthu kumneneza ndi kuti analakwa;