Deuteronomy 19:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aweruziwo adzafufuze za mlanduwo. Akapeza kuti munthu uja ndi mboni yachabe ndipo kuti waneneza mnzake monama,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo oweruza afunsitse bwino; ndipo taonani, mboniyo ikakhala mboni yonama, yomnamizira mbale wake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Oweruza afufuze bwinobwino, ndipo ngati zatsimikizika kuti mboniyo ndi yabodza, yopereka umboni wonama pa mʼbale wake,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo oweruza afunsitse bwino; ndipo taonani, mboniyo ikakhala mboni yonama, yomnamizira mbale wace;