Deuteronomy 19:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudzakonze miseu yake, ndipo mudzaligaŵe patatu dzikolo. Choncho kudzakhala malo amene munthu wopha mnzake adzatha kuthaŵirako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mudzikonzere njira, ndi kugawa malire a dziko lanu, limene Yehova Mulungu wanu akupatsani likhale lanulanu, patatu; kuti wakupha munthu athawireko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mudzakonze misewu ndi kuligawa patatu dzikolo limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani ngati cholowa chanu, kuti aliyense wopha munthu akhoza kuthawirako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mudzikonzere njira, ndi kugawa malire a dziko lanu, limene Yehova Mulungu wanu akupatsani likhale lanu lanu, patatu; kuti wakupha munthu athawireko.