Deuteronomy 19:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake ndikukulamulani kuti mupatule mizinda itatu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake ndikuuzani ndi kuti, Mudzipatulire midzi itatu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ichi ndi chifukwa chake ndikukulamulani kuti mudzipatulire nokha mizinda itatu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace ndikuuzani ndi kuti, Mudzipatulire midzi itatu.