Deuteronomy 2:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
(Kale ku Ari kunkakhala mtundu wina wa anthu otchedwa Aemimu. Anthu ake anali otchuka ndiponso ambiri. Kutalika kwao ankalingana ndi mtundu wina wa anthu otchedwa Aanaki.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
(Aemimu anakhalamo kale, ndiwo anthu akulu, ndi ambiri, ndi ataliatali, ngati Aanaki.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
(Aemi, anthu amphamvu ndi ochuluka komanso ataliatali ngati Aanaki amakhala kumeneko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
(Aemi anakhalamo kale, ndiwo anthu akuru, ndi ambiri, ndi atalitali, ngati Aanaki.