Deuteronomy 2:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Monga Aanaki omwe, anthuwo ankadziŵika ndi dzina lakuti Arefaimu. Koma Amowabu ankaŵatchula kuti Aemimu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anawayesa iwonso Arefaimu, monga Aanaki; koma Amowabu awatcha Aemimu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati Aanaki, nawonso ankawayesa kuti anali Arefai, koma Amowabu ankawatcha iwo Aemi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anawayesa iwonso Arefai, monga Aanaki; koma Amoabu awacha Aemi.