Deuteronomy 2:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
(Dziko limeneli linalinso dziko la Arefaimu, chifukwa kale iwowo ankakhala m'dziko limeneli. Aamoni ankaŵatchula kuti Azamzumimu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
(Ilinso aliyesa dziko la Arefaimu; Arefaimu anakhalamo kale; koma Aamoni awatcha Azamzumimu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
(Ilinso ankaliyesa dziko la Arefai amene ankakhala kumeneko. Koma Aamoni ankawatcha iwo Azamuzumi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
(Ilinso aliyesa dziko la Arefai; Arefai anakhalamo kale; koma Aamoni awacha Azamzumi;