Deuteronomy 2:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chakudya mudzachita chotigulitsa, madzi akumwanso mudzachita otigulitsa. Mungotilola kuti tidzere m'dziko mwanu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Undigulitse chakudya ndi ndalama, kuti ndidye; ndi kundipatsa madzi kwa ndalama, kuti ndimwe; chokhachi ndipitire choyenda pansi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mutigulitse chakudya kuti tidye ndi madzi kuti timwe pa mtengo wa siliva. Mungotilola kuti tidutse, tikuyenda pansi
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Undigulitse cakudya ndi ndarama, kuti ndidye; ndi kundipatsa madzi kwa ndarama, kuti ndimwe; cokhaci ndipitire coyenda pansi;