Deuteronomy 2:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kuti tiwoloke mtsinje wa Yordani ndi kukafika ku dziko limene Chauta, Mulungu wathu, akutipatsa. Zidzukulu za Esau ku Edomu, ndi Amowabu ku Ari, onsewo adatilola kudzera m'maiko mwao.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
monga anandichitira ana a Esau akukhala m'Seiri, ndi Amowabu akukhala m'Ari; kufikira nditaoloka Yordani kulowa dziko limene Yehova Mulungu wathu atipatsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
monga mmene anatichitira adzukulu a Esau okhala ku Seiri ndi Amowabu okhala ku Ari mpaka titawoloka Yorodani kufika ku dziko limene Yehova Mulungu wathu akutipatsa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
monga anandicitira ana a Esau akukhala m'Seiri, ndi Amoabu akukhala m'Ari; kufikira nditaoloka Yordano kulowa dziko limene Yehova Mulungu wathu atipatsa.